Skip to content
Chotitsogolera episode artwork

EPISODE · Apr 13, 2023 · 26 MIN

Chotitsogolera

from Chuma mzikho zadothi · host John Joseph Matandika

Musaganize kuti ndidadza Ine kudzapasula chilamulo kapena aneneri; sindinadza kupasula koma kukwaniritsa. Pakuti indetu ndinena kwa inu, Kufikira litapitirira thambo ndi dziko, kalemba kakang’ono kamodzi kapena kasonga kake kamodzi sikadzachoka kuchilamulo, kufikira zitachitidwa zonse. Chifukwa chake yense womasula limodzi la malamulo amenewa ang’onong’ono, nadzaphunzitsa anthu chomwecho, adzatchulidwa wamng’onong’ono mu Ufumu wa kumwamba; koma yense wochita ndi kuphunzitsa awa, iyeyu adzatchulidwa wa mkulu mu Ufumu wa kumwamba. Pakuti ndinena ndi inu, Ngati chilungamo chanu sichichuluka choposa cha alembi ndi Afarisi, simudzalowa konse mu Ufumu wa kumwamba. (Mat 5:17-20)

Episode metadata supplied by the publisher feed · Published Apr 13, 2023

Embed this episode

Ready to play

Chotitsogolera

0:00 26:40

No transcript for this episode yet

We transcribe on demand. Request one and we'll notify you when it's ready — usually under 10 minutes.

No similar episodes found.

No similar podcasts found.

Frequently Asked Questions

How long is this episode of Chuma mzikho zadothi?

This episode is 26 minutes long.

When was this Chuma mzikho zadothi episode published?

This episode was published on April 13, 2023.

Can I download this Chuma mzikho zadothi episode?

Yes. Use the download control on the episode player to save the publisher-provided media file.
URL copied to clipboard!