Skip to content
Chuma mzikho zadothi podcast artwork

PODCAST · religion

Chuma mzikho zadothi

by John Joseph Matandika

Kufalitsa uthenga wa Ambuye wathu Yesu Khristu.

Publisher-supplied feed metadata · PodParley refreshed May 25, 2022 · Source feed

Episodes

  1. Nkhondo ya Uzimu

    The LORD God said to the serpent, “Because you have done this, cursed are you above all livestock and above all beasts of the field; on your belly you shall go, and dust you shall eat all the days of your life. I will put enmity between you and the woman, and between your offspring and her...

  2. Mtengo wa Chiyero

    Ngati munthu adza kwa Ine, wosada atate wake ndi amake, ndi mkazi wake, ndi ana, ndi abale ake, ndi alongo ake, inde ndi moyo wake womwe wa iye mwini, sakhoza kukhala wophunzira wanga. Ndipo amene ali yense sasenza mtanda wake wa mwini yekha, ndi kudza pambuyo panga, sakhoza kukhala wophunzira...

  3. Kusamvetsetsa Chiyero Gawo 1

    Ndipo wophunzira a Yohane ndi Afarisi adalimkusala kudya; ndipo anadza, nanena ndi Iye, Bwanji asala kudya wophunzira a Yohane, ndi wophunzira Afarisi, koma wophunzira anu sasala kudya? Ndipo Yesu adanena nawo, Kodi akhoza kusala kudya ana a ukwati pamene mkwati ali pamodzi nawo? Pokhala ali naye...

  4. Kulungamitsidwa Mutu 2

    Monga kwalembedwa, palibe m’modzi wolungama, inde palibe m’modzi; Palibe m’modzi wakudziwitsa, palibe m’modzi wakufunafuna Mulungu; Onsewa apatuka njira, wonsewa pamodzi akhala wopanda phindu; palibe m’modzi wochita zabwino, inde, palibe m’modzi ndithu. M’mero mwawo muli manda apululu; Ndi lilime...

  5. Thandizo

    Koma pamene wafika Nkhoswe, amene Ine ndidzamtuma kwa inu kuchokera kwa Atate, ndiye Mzimu wa chowonadi amene atuluka kwa Atate, Iyeyu adzandichitira Ine umboni. Ndipo inunso mudzachitira umboni, chifukwa mudali ndi Ine kuyambira pachiyambi. (Joh 15:26-27)

  6. Kuyeretsedwa Mutu 1

    Chifukwa chake ndikupemphani inu, abale, mwa zifundo za Mulungu, kuti mupereke matupi anu nsembe yamoyo, yopatulika, yokondweretsa Mulungu, ndiko kupembedza kwanu koyenera. Ndipo musafanizidwe ndi makhalidwe apansi pano; koma mukhale wosandulika, mwa kukonzanso kwa mtima wanu, kuti mukazindikire...

  7. Chotitsogolera

    Musaganize kuti ndidadza Ine kudzapasula chilamulo kapena aneneri; sindinadza kupasula koma kukwaniritsa. Pakuti indetu ndinena kwa inu, Kufikira litapitirira thambo ndi dziko, kalemba kakang’ono kamodzi kapena kasonga kake kamodzi sikadzachoka kuchilamulo, kufikira zitachitidwa zonse. Chifukwa...

  8. Chomwe Mulungu Amatipatsa

    Monga ana womvera wosadzifanizitsanso ndi zilakolako zakale, pokhala wosadziwa inu: Komatu monga Iye wakuyitana inu ali woyera mtima, khalani inunso woyera mtima m’makhalidwe anu onse: Popeza kwalembedwa, mudzikhala woyera mtima, pakuti Ine ndine woyera mtima: (1Pe 1:14-16)

  9. Kulungamitsidwa Mutu 7

    Chifukwa chake pokhala wolungamitsidwa mwa chikhulupiriro, tikhala ndi mtendere ndi Mulungu mwa Ambuye wathu Yesu Khristu; (Rom 5:1)

  10. Kulungamitsidwa Mutu 1

    Chifukwa chake pokhala wolungamitsidwa mwa chikhulupiriro, tikhala ndi mtendere ndi Mulungu mwa Ambuye wathu Yesu Khristu; (Rom 5:1)

  11. Kulungamitsidwa Mutu 6

    Kufunikila kwa imfa ya Ambuye wathu Yesu Khristu.

  12. Kulungamitsidwa Mutu 5

    Mtanda odabwitsa wa Ambuye wathu Yesu Khristu.

  13. Umunthu wa Yesu Khristu

    PACHIYAMBI panali Mawu, ndipo Mawu adali ndi Mulungu, ndipo Mawu adali Mulungu. Awa adali pachiyambi ndi Mulungu. Zinthu zonse zidalengedwa ndi Iye; ndipo kopanda Iye sikadalengedwa kanthu kena kali konse kolengedwa. Mwa Iye mudali moyo; ndi moyowu udali kuwunika kwa anthu. Ndipo kuwunikaku...

  14. Lamulo 6

    Usaphe. EKSODO 20 Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi...

  15. Lamulo 10

    Usasirire. EKSODO 20 Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko…

    more
  16. Lamulo 8

    Usabe. EKSODO 20 Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi...

  17. Lamulo 7

    Usachite chigololo. EKSODO 20 Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa...

  18. Lamulo 9

    Usapereke umboni omunamizila mzako. EKSODO 20 Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba...

  19. Nsembe Yokwanilitsa Chilungamo cha Mulungu

    Kuzunzika ndi Ulemerero wa Mtumiki 13Taonani, mtumiki wanga adzapambana pa ntchito yake adzakwezedwa ndi kulemekezedwa ndipo adzalandira ulemu waukulu kwambiri. 14Anthu ambiri atamuona anadzidzimuka, chifukwa nkhope yake inali itasakazika; sinalinso ngati ya munthu. Ndipo thupi lake linasakazika;...

  20. Kugwa kwa Munthu

    Kuchimwa kwa Munthu 1Ndipo njoka inali yochenjera kuposa nyama yakuthengo iliyonse imene Yehova Mulungu anapanga. Njokayo inati kwa mkaziyo, “Kodi Mulungu ananenadi kuti, ‘Inu musadye zipatso za mtengo uliwonse mʼmundamu?’ ” 2Mkaziyo anati kwa njokayo, “Tikhoza kudya zipatso za mʼmitengo ya...

  21. Kulemekeza kwa Anzeru a ku M'mawa

    Ndipo pa kubadwa kwake kwa Yesu mu Betelehemu wa Yudeya m’masiku a Herode mfumu, onani, Anzeru a kum’mawa anafika ku Yerusalemu, Nanena, Ali kuti amene adabadwa mfumu ya Ayuda? Chifukwa tidawona nyenyezi yake kum’mawa, ndipo tidabwera kudzamlambira Iye. Pamene Herode mfumuyo adamva ichi…

    more
  22. Kufunikila kwa Imfa ya Ambuye Yesu

    Koma atafika Khristu, Mkulu wansembe wa zabwino ziri mkudza, mwa chihema chachikulu ndi changwiro choposa, chosamangika ndi manja, ndiko kunena kuti, chosati cha chilengedwe ichi; Kosati mwa mwazi wa mbuzi ndi ana ang’ombe, koma mwa mwazi wa Iye yekha, adalowa kamodzi kumalo wopatulika,...

  23. Mtanda Odabwitsa

    Ndipo pomwepo m`mawa adakhala upo ansembe akulu, ndi akulu a anthu, ndi alembi, ndi akulu a milandu onse, namanga Yesu, namtenga, nampereka kwa Pilato. Ndipo Pilato adamfunsa Iye, Kodi ndiwe Mfumu ya Ayuda? Ndipo poyankha adati kwa iye, Mwatero ndinu. Ndipo ansembe akulu adamnenera Iye zinthu...

  24. Kubadwa mwa Namwali Kodabwitsa

    Tsoka kwa inu, pamene anthu adzanenera inu zabwino! Pakuti makolo awo adawatero momwemo aneneri wonama. Koma ndinena kwa inu akumva, kondanani nawo adani anu; chitirani zabwino iwo akuda inu. Dalitsani iwo akutemberera inu, pemphererani iwo akuchitira inu chipongwe. Ndipo kwa Iye amene akupanda…

    more
  25. Zochitika pa Kubadwa kwa Yesu

    Ambuye wathu Yesu Khristu anabadwa modabwitsa. Luka 2:1-7 Ndipo kudali masiku aja, kuti lamulo lidatuluka kwa Kayisala Augusto kuti dziko lonse lokhalamo anthu lilembedwe. Ndiko kulembera koyamba pokhala Kureniyo kazembe wa Suriya. Ndipo onse adapita kukalembedwa, munthu aliyense ku mzinda wake....

  26. Lamulo Lachisanu

    Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi…

    more
  27. Lamulo Lachinayi

    Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi…

    more
  28. Malamulo Khumi Gawo 2

    Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi…

    more
  29. Malamulo Khumi Gawo 1

    Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi…

    more
  30. Udindo wa Munthu

    Malamulo Khumi 1Ndipo Mulungu anayankhula mawu onse awa nati: 2“Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakutulutsa ku Igupto, mʼdziko la ukapolo. 3“Usakhale ndi milungu ina koma Ine ndekha.” 4“Usadzipangire chofanizira chinthu chilichonse chakumwamba kapena cha pa dziko lapansi kapena cha mʼmadzi…

    more
  31. Kubadwa kwa Yohane

    Aneneratu za Kubadwa kwa Yohane Mʼbatizi 5Mʼmasiku a Herode, mfumu ya Yudeya, kunali wansembe dzina lake Zakariya wa gulu la ansembe la Abiya; mkazi wake Elizabeti analinso wa fuko la Aaroni. 6Onse awiri anali olungama pamaso pa Mulungu, ndipo amasunga malamulo ndi malangizo onse a Ambuye…

    more
  32. Kubadwa kwa Yesu

    Makolo a Yesu Khristu Monga mwa Thupi 1Buku lofotokoza za mʼbado wa Yesu Khristu mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu: 2Abrahamu anabereka Isake, Isake anabereka Yakobo, Yakobo anabereka Yuda ndi abale ake. 3Yuda anabereka Perezi ndi Zara, amene amayi awo anali Tamara. Perezi anabereka Hezironi,...

  33. Tanthauzo la Pemphero Gawo Lomaliza

    Salimo 100 1Fuwulani kwa Yehova mwachimwemwe, inu dziko lonse lapansi. 2Mulambireni Yehova mosangalala; bwerani pamaso pake ndi nyimbo zachikondwerero. 3Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu. Iye ndiye amene anatipanga ndipo ife ndife ake; ndife anthu ake, nkhosa za pabusa pake. 4Lowani ku zipata zake...

  34. Kusala ndi Kulapa

    Eksodo 34:28 Mose anakhala kumeneko pamodzi ndi Yehova masiku 40, usana ndi usiku, wosadya kanthu kapena kumwa madzi. Ndipo iye analemba pa miyala ija mawu a pangano, malamulo khumi. Machitidwe 27:9 Tinataya nthawi yayitali, ndipo kuyenda pa nyanja kunali koopsa chifukwa nʼkuti tsopano nthawi...

  35. Mapemphero Ena

    Mateyu 26:36-46 36Kenaka Yesu anapita ku malo otchedwa Getsemani, ndipo anawawuza kuti, “Khalani pano pamene Ine ndikukapemphera apo.” 37Anatenga Petro ndi ana awiri a Zebedayo, ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika mu mtima. 38Pamenepo anawawuza kuti, “Moyo wanga uli ndi chisoni chofa nacho....

  36. Pemphero la Ambuye Gawo 2

    9 “Chifukwa chake pempherani motere: “ ‘Atate athu akumwamba, dzina lanu lilemekezedwe, 10 Ufumu wanu ubwere, chifuniro chanu chichitike pansi pano monga kumwamba. 11 Mutipatse chakudya chathu chalero. 12 Mutikhululukire mangawa athu, monga ifenso tawakhululukira amangawa athu. 13 Ndipo...

  37. Pemphero la Ambuye

    Mateyu 6:9-13 9 “Chifukwa chake pempherani motere: “ ‘Atate athu akumwamba, dzina lanu lilemekezedwe, 10 Ufumu wanu ubwere, chifuniro chanu chichitike pansi pano monga kumwamba. 11 Mutipatse chakudya chathu chalero. 12 Mutikhululukire mangawa athu, monga ifenso tawakhululukira amangawa athu. 13...

  38. Tipemphere Nthawi Yanji? Gawo 2

    Salimo 145:1-3 1Ndidzakukwezani Mulungu wanga, Mfumu yanga; ndidzatamanda dzina lanu ku nthawi za nthawi. 2Ndidzakutamandani tsiku ndi tsiku ndi kulemekeza dzina lanu ku nthawi za nthawi. 3Yehova ndi wamkulu ndi woyenera matamando onse; ukulu wake palibe angawumvetsetse.

  39. Tipemphere Nthawi Yanji?

    Machitidwe 2:42-47 42Iwo ankasonkhana pamodzi kuphunzitsidwa ndi atumwi, pachiyanjano, pachakudya ndi popemphera. 43Aliyense ankachita mantha chifukwa cha zodabwitsa ndi zizindikiro zambiri zimene atumwi ankachita. 44Okhulupirira onse anali pamodzi ndipo aliyense ankapereka zinthu zake kuti…

    more
  40. Tipemphere Chifukwa Chiyani?

    LUKA 11 Yesu Aphunzitsa za ku Pemphera 1Tsiku lina Yesu amapemphera pamalo ena. Atamaliza, mmodzi wa ophunzira ake anati kwa Iye, “Ambuye tiphunzitseni kupemphera, monga momwe Yohane anaphunzitsira ophunzira ake.” 2Yesu anawawuza kuti, “Pamene mukupemphera muzinena kuti: “ ‘Atate, dzina lanu...

  41. Magawo a Pemphero Gawo 2

    MASALIMO 3 Salimo la Davide. Atathawa mwana wake Abisalomu. 1Inu Yehova, achulukadi adani anga! Achulukadi amene andiwukira! 2Ambiri akunena za ine kuti, “Mulungu sadzamupulumutsa.” Sela 3Koma Inu Yehova, ndinu chishango chonditeteza, Inu mwandiveka ulemerero ndipo mwanditukula. 4Kwa Yehova, Ine...

  42. Magawo a Pemphero

    MASALIMO 136 1Yamikani Yehova chifukwa ndi wabwino. Pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. 2Yamikani Mulungu wa milungu. Pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. 3Yamikani Ambuye wa ambuye, pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya. 4Iye yekhayo amene amachita zodabwitsa...

  43. Tanthauzo la Pemphero

    Aroma 8:26-28 26Momwemonso, Mzimu amatithandiza ife mʼkufowoka kwathu. Ife sitidziwa momwe tiyenera kupempherera koma Mzimu mwini amatipempherera mobuwula ndi mawu osafotokozedwa. 27Koma Iye amene amasanthula mitima yathu amadziwa maganizo a Mzimu, chifukwa Mzimu amapempherera oyera mtima…

    more
  44. Kodi tipemphere motani?

    Mateyu 6:5-8 5 “Pamene mupemphera, musakhale ngati achiphamaso, chifukwa iwo amakonda kupemphera choyimirira mʼmasunagoge ndi pa mphambano za mʼmisewu kuti anthu awaone. Zoonadi, Ine ndikuwuzani kuti iwo alandiriratu mphotho yawo yonse. 6Koma pamene mupemphera, lowani mʼchipinda chanu chamʼkati,...

  45. Kukondana Wina ndi Mnzake

    Mateyu 25:34-40 34 “Pamenepo mfumu idzati kwa a ku dzanja lamanja, ‘Bwerani inu odalitsika ndi Atate anga; landirani ufumu umene unakonzedwa chifukwa cha inu kuyambira pachiyambi cha dziko. 35Pakuti ndinali ndi njala ndipo munandipatsa chakudya, ndinali ndi ludzu ndipo munandipatsa madzi akumwa,...

  46. Kubwezana Tikalowelera

    Patokha timalowelera Galatians 6:1 Abale, ngati munthu agwa mʼtchimo lililonse, inu amene Mzimu amakutsogolerani, mumuthandize munthuyo ndi mtima wofatsa kuti akonzekenso. Koma mukhale maso kuti inu nomwe mungayesedwe. Yakobo 15:19-20 19Abale anga, ngati mmodzi wa inu apatuka pa choonadi ndipo…

    more
  47. Kuphuzila kukonda Akhristu azathu

    Lero tikupitiliza kulingalira zifukwa zimene tikusowekela kukhala pa mpingo. Sabata yatha, tidayamba kuyankha funso limeneli pakunena kuti tikusowekela mpingo popeza kuti timayanjanitsidwa ndi okhulupilira ena mwa Khristu komanso popeza timakula pamodzi kufikila kukula mwa Khristu ndi…

    more
  48. Kuyanjanitsidwa ndi Khristu

    Lero tikufuna tione za kuyanjanitsidwa ndi Khristu komanso kukula pamodzi. Funso limene tingayambe nalo ndi lakuti; ndi chifukwa chiyani tikusowekela mpingo m’moyo mwathu? Masabata akubwela kutsogolowa tikhala tikuona kuti pali zifukwa zingapo zimene tikusowekela mpingo m’moyo mwathu. Sabata ino,...

  49. Kukhala Membala Pa Mpingo

    Lero tikufuna tione za kukhala membala pa mpingo Chiyambileni kuona za mpingo takhala tikuona za tanthauzo la mpingo komanso m’mene umagwilira ntchito. Koma zimatheka kuti anthu ambiri atha kumapemphela ndi anzawo pa mpingo koma sadutsa njira zimene zimafunikila kuti akhale membala wodziwika pa...

  50. Chikhalidwe Komanso Tanthauzo la Ubatizo

    Tipite ku nkhani ya lero: chikhalidwe komanso tanthauzo la ubatizo. Tikuyenela tizindikile kuti nkhani ya ubatizo ndi nkhani imene yabweletsa mpungwepungwe pakati pa mipingo. Ndipo pena zimakhala zovetsa chisoni kuti akhristu amapezeka kuti akugawanikana pa nkhani imeneyi. Kusiyana kwathu pa…

    more

Type above to search every episode's transcript for a word or phrase. Matches are scoped to this podcast.

Searching…

We're indexing this podcast's transcripts for the first time — this can take a minute or two. We'll show results as soon as they're ready.

No matches for "" in this podcast's transcripts.

Showing of matches

No topics indexed yet for this podcast.

Loading reviews...

ABOUT THIS SHOW

Kufalitsa uthenga wa Ambuye wathu Yesu Khristu.

HOSTED BY

John Joseph Matandika

Frequently Asked Questions

How many episodes does Chuma mzikho zadothi have?

Chuma mzikho zadothi currently has 58 episodes available on PodParley. New episodes are automatically indexed when they're published to the podcast feed.

What is Chuma mzikho zadothi about?

Kufalitsa uthenga wa Ambuye wathu Yesu Khristu.

How often does Chuma mzikho zadothi release new episodes?

Chuma mzikho zadothi has 58 episodes. Check the episode list to see recent publication dates and frequency.

Where can I listen to Chuma mzikho zadothi?

You can listen to Chuma mzikho zadothi on PodParley by clicking any episode. We provide an embedded audio player for direct listening, and you can also subscribe via your preferred podcast app using the RSS feed.

Who hosts Chuma mzikho zadothi?

Chuma mzikho zadothi is created and hosted by John Joseph Matandika.
URL copied to clipboard!