Skip to content
Mtengo wa Chiyero episode artwork

Apr 13, 2023 27 min

Mtengo wa Chiyero

from Chuma mzikho zadothi Hosted by John Joseph Matandika

Ngati munthu adza kwa Ine, wosada atate wake ndi amake, ndi mkazi wake, ndi ana, ndi abale ake, ndi alongo ake, inde ndi moyo wake womwe wa iye mwini, sakhoza kukhala wophunzira wanga. Ndipo amene ali yense sasenza mtanda wake wa mwini yekha, ndi kudza pambuyo panga, sakhoza kukhala wophunzira wanga. Pakuti ndani wa inu amene akufuna kumanga nsanja yayitali, sayamba wakhala pansi, nawerengera mtengo wake, awone ngati ali nazo zakuyimaliza? Kuti kungachitike, pamene atakhazika pansi miyala ya maziko ake, wosakhoza kuyimaliza, anthu onse woyang’ana adzayamba kumseka iye. Ndikunena kuti, Munthu uyu adayamba kumanga, koma sadathe kumaliza. Kapena mfumu yanji pakupita kukomana ndi nkhondo ya mfumu imzake, siyiyamba yakhala pansi, nafunsana ndi akulu ngati akhoza ndi asilikari ake zikwi khumi kulimbana naye wina uja alikudza kukomana naye ndi asilikari zikwi makumi awiri? Koma ngati sakhoza, atumiza akazembe, pokhala winayo ali kutalitali, nafunsa za mtendere. Chomwecho ndinena kwa inu, yense wa inu amene sakaniza zonse ali nazo, sakhoza kukhala wophunzira wanga. (Luk 14:26-33)

Episode details come from the podcast's RSS feed.

Embed this episode

Ready to play

Mtengo wa Chiyero

0:00 27:19

No transcript yet.

Requests help us decide what to transcribe next.

Frequently asked questions

How long is this episode of Chuma mzikho zadothi?

This episode is 27 minutes long.

When was this Chuma mzikho zadothi episode published?

This episode was published on April 13, 2023.

Can I download this Chuma mzikho zadothi episode?

Yes. Use the download control on the episode player to save the publisher-provided media file.