EPISODE · Oct 27, 2021 · 27 MIN
Pemphero la Ambuye
from Chuma mzikho zadothi · host John Joseph Matandika
Mateyu 6:9-13 9 “Chifukwa chake pempherani motere: “ ‘Atate athu akumwamba, dzina lanu lilemekezedwe, 10 Ufumu wanu ubwere, chifuniro chanu chichitike pansi pano monga kumwamba. 11 Mutipatse chakudya chathu chalero. 12 Mutikhululukire mangawa athu, monga ifenso tawakhululukira amangawa athu. 13 Ndipo musatitengere kokatiyesa; koma mutipulumutse kwa woyipayo.’
Embed this episode
Ready to play
Pemphero la Ambuye
No transcript for this episode yet
Similar Episodes
No similar episodes found.
Similar Podcasts
No similar podcasts found.