Skip to content
Tanthauzo la Pemphero episode artwork

Sep 18, 2021 27 min

Tanthauzo la Pemphero

from Chuma mzikho zadothi Hosted by John Joseph Matandika

Aroma 8:26-28 26Momwemonso, Mzimu amatithandiza ife mʼkufowoka kwathu. Ife sitidziwa momwe tiyenera kupempherera koma Mzimu mwini amatipempherera mobuwula ndi mawu osafotokozedwa. 27Koma Iye amene amasanthula mitima yathu amadziwa maganizo a Mzimu, chifukwa Mzimu amapempherera oyera mtima molingana ndi chifuniro cha Mulungu. 28Ndipo ife tikudziwa kuti zinthu zonse zimathandizana kuwachitira ubwino amene amakonda Mulungu, amene anayitanidwa monga mwa cholinga chake.

Episode details come from the podcast's RSS feed.

Embed this episode

Ready to play

Tanthauzo la Pemphero

0:00 27:40

No transcript yet.

Requests help us decide what to transcribe next.

Frequently asked questions

How long is this episode of Chuma mzikho zadothi?

This episode is 27 minutes long.

When was this Chuma mzikho zadothi episode published?

This episode was published on September 18, 2021.

Can I download this Chuma mzikho zadothi episode?

Yes. Use the download control on the episode player to save the publisher-provided media file.