Skip to content
Tipemphere Chifukwa Chiyani? episode artwork

Oct 7, 2021 31 min

Tipemphere Chifukwa Chiyani?

from Chuma mzikho zadothi Hosted by John Joseph Matandika

LUKA 11 Yesu Aphunzitsa za ku Pemphera 1Tsiku lina Yesu amapemphera pamalo ena. Atamaliza, mmodzi wa ophunzira ake anati kwa Iye, “Ambuye tiphunzitseni kupemphera, monga momwe Yohane anaphunzitsira ophunzira ake.” 2Yesu anawawuza kuti, “Pamene mukupemphera muzinena kuti: “ ‘Atate, dzina lanu lilemekezedwe, ufumu wanu ubwere. 3 Mutipatse chakudya chathu chalero, 4 mutikhululukire machimo athu, monga ifenso timakhululukira aliyense amene watilakwira. Ndipo musalole kuti tigwe mʼmayesero.’ ”

Episode details come from the podcast's RSS feed.

Embed this episode

Ready to play

Tipemphere Chifukwa Chiyani?

0:00 31:56

No transcript yet.

Requests help us decide what to transcribe next.

Frequently asked questions

How long is this episode of Chuma mzikho zadothi?

This episode is 31 minutes long.

When was this Chuma mzikho zadothi episode published?

This episode was published on October 7, 2021.

Can I download this Chuma mzikho zadothi episode?

Yes. Use the download control on the episode player to save the publisher-provided media file.